From April 24th to 25th, 2025, Civil Society Organizations (CSOs) came together for an impactful training on Climate Change Management and Climate …
Monthly Archives
April 2025
-
Uncategorized
-
-
-
Uncategorized
Phungu wakumwera m’boma la Ntchisi a Ulemu Chilapondwa lero akawonekera ku komiti yayikulu ya chipani cha Malawi Congress Party MCP ya m’bomali powonetsa chidwi choyima nawo pachisankho chachipulura chomwe chichitike posachedwapa.
by Clary Simionby Clary SimionPolankhula atalandilidwa phunguyu anati ndiwokondwa kuti chipani chamulandila mwasangala iwo anawonjezera kuti akapanga kampeni yabata kuti akapambane pachisankho chachipulura ndikudzayima patikiti ya …
-
-
-
-
Uncategorized
Bungwe la NGO Gender Coordination Network Lero likuchititsa maphunziro a tsiku limodzi ndi Atolankhani a M’boma la Ntchisi pofuna kulimbikitsa amayi kutenga nawo mbali pa masankho Mdziko la Malawi.
by Clary Simionby Clary SimionMaphuzilowa akuchitikila Ku Ntchisi Executive lodge ndipo ena omwe atenga nawo mbali ndi atolankhani a Ntchisi Youth FM ,Times,Zodiak and Malawi News …
-
Uncategorized
Olemekeza a Ulemu Chilapondwa ayamba ndikupepesa a Peter Gamula kamba kotaya agogo awo dzulo ndipo alowa m’manda lero.
by Clary Simionby Clary Simion“Poyamba ndisanayambe zonse ndikufuna ndipepese m’modzi mwa anthu omwe akufuna kupikisana nawo kuno a Peter Gamula kamba kotaya agogo awo dzulo omwe …
-
Uncategorized
Mlembi wa mkulu wa chipani cha Malawi Congress Party MCP a Richard Chimwendo Banda apempha anthu m’boma la Ntchisi kuti adzavotere a Dr Chakwera pamasankho omwe aliko pa 16 September 2025.
by Clary Simionby Clary SimionIwo anati boma la a Chakwera lachita zitukuko zambili monga kumanga misewu,kumanga zipinda zophuziliramo komanso kumanga nyumba za apolisi kungotchulako zochepa chabe. …
Newer Posts