Owatsatira awo, a Joseph Manguluti apeza mavoti okwana 112 ndipo a Vasco Ntunduwatha Chimbalu apeza mavoti 35. Izi zikutanthauza kuti a Chithyola …
Monthly Archives
April 2025
-
-
Uncategorized
Dr Joyce Banda yemwe ndi mtsogoleri wachipani cha Peoples Party(PP) apempha anthu ochuluka omwe asonkhana pa Masangano primary School ground m’boma la Ntchisi kuti adzawavotere pamasankho omwe achitike pa 16 September 2025.
by Clary Simionby Clary SimionIwo anati nthawi yomwe anayendetsa dziko lino zinthu zinali pabwino pomwe wati nthawi yake anagawa ng’ombe,kubwezeletsa Chuma mchimake,kugawa njinga zamoto komanso anthu …
Older Posts