Home Business MWAMBO WA CHIWONETSERO CHA ZA ULIMI M’BOMA LA NTCHISI ULI MKATI

MWAMBO WA CHIWONETSERO CHA ZA ULIMI M’BOMA LA NTCHISI ULI MKATI

by Clary Simion
0 comments

MWAMBO WA CHIWONETSERO CHAZAULIMI ULIMKATI M’BOMA LA NTCHISI

Mwambo wa chionetsero cha zaulimi m’boma la Ntchisi uli mkati m’dera la Mfumu yaikulu Kalumo, m’mudzi mwa Kanyenda ku Chipuka Extension Planning Area (EPA).

Mwambowu ukuchitika pa mutu wakuti, “Kuchita ulimi ndi malonda a kasakaniza ndi njira imodzi yochepetsera zotsatira za Kusintha kwa nyengo pa banja komanso Ku dera”.

Mlendo olemekezeka pa mwambowu ndi District Council Chair Mr Mark Mphenzi Mtengo.

Olemba: Deborah Chuma (27th March, 2025)

NY FM Mphamvu kwa mzika

Leave a Comment

Dowa Community Radio is a community-based radio station established in 2020 to be used as a tool of communication in Dowa district and surrounding areas to facilitate issues of Education, gender-based violence, culture, child trafficking, Agriculture, Climate change and environment, transparency and accountability, sports, community self reliance, and many more.

Newsletter

Subscribe my Newsletter for new blog posts, tips & new photos. Let's stay updated!

@2025 – All Right Reserved. MACRA Community Radios

Are you sure want to unlock this post?
Unlock left : 0
Are you sure want to cancel subscription?
-
00:00
00:00
Update Required Flash plugin
-
00:00
00:00