Home Uncategorized Dr Joyce Banda yemwe ndi mtsogoleri wachipani cha Peoples Party(PP) apempha anthu ochuluka omwe asonkhana pa Masangano primary School ground m’boma la Ntchisi kuti adzawavotere pamasankho omwe achitike pa 16 September 2025.

Dr Joyce Banda yemwe ndi mtsogoleri wachipani cha Peoples Party(PP) apempha anthu ochuluka omwe asonkhana pa Masangano primary School ground m’boma la Ntchisi kuti adzawavotere pamasankho omwe achitike pa 16 September 2025.

by Clary Simion
0 comments

Iwo anati nthawi yomwe anayendetsa dziko lino zinthu zinali pabwino pomwe wati nthawi yake anagawa ng’ombe,kubwezeletsa Chuma mchimake,kugawa njinga zamoto komanso anthu samagona ndi njala zomwe wati nthawi yakwana kuti anthu amuyike pampando pakuti kagwilidwe kantchitoyi akuyidziwa.

Ndipo iwo ati adziwonera okha pomwe amabwela kuti chimanga m’minda mulibe zomwe zikusonyezelatu kuti m’boma la Ntchisi kukhala njala yadzawoneni.

Olemba: Chifuniro Chikaphonya (06 April 2025)

#NY FM mphanvu kwa mzika#

You may also like

Leave a Comment

Dowa Community Radio is a community-based radio station established in 2020 to be used as a tool of communication in Dowa district and surrounding areas to facilitate issues of Education, gender-based violence, culture, child trafficking, Agriculture, Climate change and environment, transparency and accountability, sports, community self reliance, and many more.

Newsletter

Subscribe my Newsletter for new blog posts, tips & new photos. Let's stay updated!

@2025 – All Right Reserved. MACRA Community Radios

Are you sure want to unlock this post?
Unlock left : 0
Are you sure want to cancel subscription?
-
00:00
00:00
Update Required Flash plugin
-
00:00
00:00