Home Uncategorized A Simplex Chithyola Banda, ndi omwe apambana pa chisankho cha chipulura cha dera la Kumwera kwa boma la Kasungu atapeza ma voti okwana 2216.

A Simplex Chithyola Banda, ndi omwe apambana pa chisankho cha chipulura cha dera la Kumwera kwa boma la Kasungu atapeza ma voti okwana 2216.

by Clary Simion
0 comments

Owatsatira awo, a Joseph Manguluti apeza mavoti okwana 112 ndipo a Vasco Ntunduwatha Chimbalu apeza mavoti 35.

Izi zikutanthauza kuti a Chithyola Banda ndi amene adzaimire ngati phungu wa derali mchipani cha MCP.

Nthumwi zokwana 2,615 ndi zomwe zinaponya voti.

Wolemba: Nelson Gonjani.

You may also like

Leave a Comment

Dowa Community Radio is a community-based radio station established in 2020 to be used as a tool of communication in Dowa district and surrounding areas to facilitate issues of Education, gender-based violence, culture, child trafficking, Agriculture, Climate change and environment, transparency and accountability, sports, community self reliance, and many more.

Newsletter

Subscribe my Newsletter for new blog posts, tips & new photos. Let's stay updated!

@2025 – All Right Reserved. MACRA Community Radios

Are you sure want to unlock this post?
Unlock left : 0
Are you sure want to cancel subscription?
-
00:00
00:00
Update Required Flash plugin
-
00:00
00:00