Iwo anati boma la a Chakwera lachita zitukuko zambili monga kumanga misewu,kumanga zipinda zophuziliramo komanso kumanga nyumba za apolisi kungotchulako zochepa chabe. …
Author
Clary Simion
-
-
Uncategorized
A Simplex Chithyola Banda, ndi omwe apambana pa chisankho cha chipulura cha dera la Kumwera kwa boma la Kasungu atapeza ma voti okwana 2216.
by Clary Simionby Clary SimionOwatsatira awo, a Joseph Manguluti apeza mavoti okwana 112 ndipo a Vasco Ntunduwatha Chimbalu apeza mavoti 35. Izi zikutanthauza kuti a Chithyola …
-
Uncategorized
Dr Joyce Banda yemwe ndi mtsogoleri wachipani cha Peoples Party(PP) apempha anthu ochuluka omwe asonkhana pa Masangano primary School ground m’boma la Ntchisi kuti adzawavotere pamasankho omwe achitike pa 16 September 2025.
by Clary Simionby Clary SimionIwo anati nthawi yomwe anayendetsa dziko lino zinthu zinali pabwino pomwe wati nthawi yake anagawa ng’ombe,kubwezeletsa Chuma mchimake,kugawa njinga zamoto komanso anthu …
-
Uncategorized
Tiyembekeze kukhala ndi chisankho cha mtendere, Mkulu wa NICE ku Ntchisi watelo.
by Clary Simionby Clary SimionMkulu wa bungwe la National Initiative for Civic Education NICE wa m’boma la Ntchisi a Adam Disi ati bungwe lawo ndilokozeka kuphuzitsa …
-
Business
MWAMBO WA CHIWONETSERO CHA ZA ULIMI M’BOMA LA NTCHISI ULI MKATI
by Clary Simionby Clary SimionMWAMBO WA CHIWONETSERO CHAZAULIMI ULIMKATI M’BOMA LA NTCHISI Mwambo wa chionetsero cha zaulimi m’boma la Ntchisi uli mkati m’dera la Mfumu yaikulu …
Older Posts