Home Uncategorized Bungwe la NGO Gender Coordination Network Lero likuchititsa maphunziro a tsiku limodzi ndi Atolankhani a M’boma la Ntchisi pofuna kulimbikitsa amayi kutenga nawo mbali pa masankho Mdziko la Malawi.

Bungwe la NGO Gender Coordination Network Lero likuchititsa maphunziro a tsiku limodzi ndi Atolankhani a M’boma la Ntchisi pofuna kulimbikitsa amayi kutenga nawo mbali pa masankho Mdziko la Malawi.

by Clary Simion
0 comments

Maphuzilowa akuchitikila Ku Ntchisi Executive lodge ndipo ena omwe atenga nawo mbali ndi atolankhani a Ntchisi Youth FM ,Times,Zodiak and Malawi News Agency (MANA)

Ndipo maphunziro akonzedwa ndi thandizo lochokera ku UN Women mothandizana ndi EU, FCDO ndi boma la UK komaso embase ya Ireland ndi Norway.

Olemba: Deborah Chuma (13 April 2025)

NY FM Mphamvu kwa mzika

You may also like

Leave a Comment

Dowa Community Radio is a community-based radio station established in 2020 to be used as a tool of communication in Dowa district and surrounding areas to facilitate issues of Education, gender-based violence, culture, child trafficking, Agriculture, Climate change and environment, transparency and accountability, sports, community self reliance, and many more.

Newsletter

Subscribe my Newsletter for new blog posts, tips & new photos. Let's stay updated!

@2025 – All Right Reserved. MACRA Community Radios

Are you sure want to unlock this post?
Unlock left : 0
Are you sure want to cancel subscription?
-
00:00
00:00
Update Required Flash plugin
-
00:00
00:00