MWAMBO WA CHIWONETSERO CHAZAULIMI ULIMKATI M’BOMA LA NTCHISI
Mwambo wa chionetsero cha zaulimi m’boma la Ntchisi uli mkati m’dera la Mfumu yaikulu Kalumo, m’mudzi mwa Kanyenda ku Chipuka Extension Planning Area (EPA).
Mwambowu ukuchitika pa mutu wakuti, “Kuchita ulimi ndi malonda a kasakaniza ndi njira imodzi yochepetsera zotsatira za Kusintha kwa nyengo pa banja komanso Ku dera”.
Mlendo olemekezeka pa mwambowu ndi District Council Chair Mr Mark Mphenzi Mtengo.
Olemba: Deborah Chuma (27th March, 2025)
NY FM Mphamvu kwa mzika