Home Uncategorized Olemekeza a Ulemu Chilapondwa ayamba ndikupepesa a Peter Gamula kamba kotaya agogo awo dzulo ndipo alowa m’manda lero.

Olemekeza a Ulemu Chilapondwa ayamba ndikupepesa a Peter Gamula kamba kotaya agogo awo dzulo ndipo alowa m’manda lero.

by Clary Simion
0 comments

“Poyamba ndisanayambe zonse ndikufuna ndipepese m’modzi mwa anthu omwe akufuna kupikisana nawo kuno a Peter Gamula kamba kotaya agogo awo dzulo omwe alowa m’manda posachedwapa”,anatero a Chilapondwa.

A Peter Gamula ndi m’modzi mwa anthu omwe akuyembekezeka kupikisana ndi a Ulemu Chilapondwa kudera la Ntchisi South Constituency.

Popitilira a Chilapondwa anati iwo ndi okondwa tsopano kuti ntchito yomanga msewu wa Malomo -Ntchisi -Dzaleka road ulimakati,komanso anati iye nthawi yomwe ali phungu wa Congress wapanga zitukuko zambili mwazina ndi ma ularo odutsa 30.

Olemba: Chifuniro Chikaphonya

spɐ puɐ sʇɥƃısuı əəS

ʇsod ʇsooq

:suoıʇɔɐəɹ llɐ

22

You may also like

Leave a Comment

Dowa Community Radio is a community-based radio station established in 2020 to be used as a tool of communication in Dowa district and surrounding areas to facilitate issues of Education, gender-based violence, culture, child trafficking, Agriculture, Climate change and environment, transparency and accountability, sports, community self reliance, and many more.

Newsletter

Subscribe my Newsletter for new blog posts, tips & new photos. Let's stay updated!

@2025 – All Right Reserved. MACRA Community Radios

Are you sure want to unlock this post?
Unlock left : 0
Are you sure want to cancel subscription?
-
00:00
00:00
Update Required Flash plugin
-
00:00
00:00