A Simplex Chithyola Banda, ndi omwe apambana pa chisankho cha chipulura cha dera la Kumwera kwa boma la Kasungu atapeza ma voti okwana 2216.
Owatsatira awo, a Joseph Manguluti apeza mavoti okwana 112 ndipo a Vasco Ntunduwatha Chimbalu apeza mavoti 35. Izi zikutanthauza kuti a Chithyola…