Bugwe la Muslim Association of Malawi (MAMU) linayitanitsa mkumano wa adindo osiyanasiyana ogwila ntchito zaboma komanso kudela kuphatikizapo achinyamata ndi cholinga chakambilana khani zauchembele wabwino komanso ubeleki.
M’mawu ake mkulu oyang’anira nkhani za uchembere komanso ubereki wabwino ku bungwe la MAMU a Francis Nyasulu, wati bungwe lawo linachiona chinthu…