Ntchisi FM
  • Home
  • Featured
  • Politics
  • Business
  • Entertainment
  • Lifestyle
  • Sports
  • About Us
  • Contact
  • Login
  • Ntchisi FM

    Bugwe la Muslim Association of Malawi (MAMU) linayitanitsa mkumano wa adindo osiyanasiyana ogwila ntchito zaboma komanso kudela kuphatikizapo achinyamata ndi cholinga chakambilana khani zauchembele wabwino komanso ubeleki.

    Ntchisi Organization for Youth and Development (NOYD) in partnership with Save the Children International with funding from SIDA facilitated and supported Review Meeting on the Resolutions made during 2024 Ntchisi District Children’s Parliament Session. The meeting aimed at assessing the achievements by various duty bearers in the district. The meeting was conducted from 25th to 26th April, 2025 at Ntchisi Executive Lodge, Ntchisi.The duty bearers were the District Commissioner, 2 Senior Traditional Authorities, Malenga and Kalumo, District Council Chairperson and Heads of various sectors like Education, Forestry, Labour, Social Welfare as key respondents.During the meeting 20 Child Members of Parliament attended representing other Child Parliamentarians across the district.Major issues raised were Child Labour, Inadequate bursary support to needy students, unfriendly disability infrastructures in schools and Environment and Climate Change as a Child Rights issue with focus on depletion of trees for charcoal making.The house finally found that many issues from 2024 Child Parliament Resolutions were not solved by duty bearers. Therefore, the meeting agreed to table the unsolved issues in the 2025 Child Parliament Session.Ntchisi District Council

    Mlembi wa mkulu wa chipani cha Malawi Congress Party MCP a Richard Chimwendo Banda apempha anthu m’boma la Ntchisi kuti adzavotere a Dr Chakwera pamasankho omwe aliko pa 16 September 2025.

    Clary SimionApril 15, 20250164 views

    Iwo anati boma la a Chakwera lachita zitukuko zambili monga kumanga misewu,kumanga zipinda zophuziliramo komanso kumanga nyumba za apolisi kungotchulako zochepa chabe.…

    Read more

    A Simplex Chithyola Banda, ndi omwe apambana pa chisankho cha chipulura cha dera la Kumwera kwa boma la Kasungu atapeza ma voti okwana 2216.

    Clary SimionApril 8, 20250130 views

    Owatsatira awo, a Joseph Manguluti apeza mavoti okwana 112 ndipo a Vasco Ntunduwatha Chimbalu apeza mavoti 35. Izi zikutanthauza kuti a Chithyola…

    Read more

    Dr Joyce Banda yemwe ndi mtsogoleri wachipani cha Peoples Party(PP) apempha anthu ochuluka omwe asonkhana pa Masangano primary School ground m’boma la Ntchisi kuti adzawavotere pamasankho omwe achitike pa 16 September 2025.

    Clary SimionApril 8, 20250100 views

    Iwo anati nthawi yomwe anayendetsa dziko lino zinthu zinali pabwino pomwe wati nthawi yake anagawa ng’ombe,kubwezeletsa Chuma mchimake,kugawa njinga zamoto komanso anthu…

    Read more

    Tiyembekeze kukhala ndi chisankho cha mtendere, Mkulu wa NICE ku Ntchisi watelo.

    Clary SimionMarch 28, 20250140 views

    Mkulu wa bungwe la National Initiative for Civic Education NICE wa m’boma la Ntchisi a Adam Disi ati bungwe lawo ndilokozeka kuphuzitsa…

    Read more

    MWAMBO WA CHIWONETSERO CHA ZA ULIMI M’BOMA LA NTCHISI ULI MKATI

    Clary SimionMarch 27, 20250142 views

    MWAMBO WA CHIWONETSERO CHAZAULIMI ULIMKATI M’BOMA LA NTCHISI Mwambo wa chionetsero cha zaulimi m’boma la Ntchisi uli mkati m’dera la Mfumu yaikulu…

    Read more

    Posts navigation

    1 2
    View Desktop Version

    Powered by PenciDesign

    Back To Top