Mlembi wa mkulu wa chipani cha Malawi Congress Party MCP a Richard Chimwendo Banda apempha anthu m’boma la Ntchisi kuti adzavotere a Dr Chakwera pamasankho omwe aliko pa 16 September 2025.
Iwo anati boma la a Chakwera lachita zitukuko zambili monga kumanga misewu,kumanga zipinda zophuziliramo komanso kumanga nyumba za apolisi kungotchulako zochepa chabe.…