Maphuzilowa akuchitikila Ku Ntchisi Executive lodge ndipo ena omwe atenga nawo mbali ndi atolankhani a Ntchisi Youth FM ,Times,Zodiak and Malawi News Agency (MANA)
Ndipo maphunziro akonzedwa ndi thandizo lochokera ku UN Women mothandizana ndi EU, FCDO ndi boma la UK komaso embase ya Ireland ndi Norway.
Olemba: Deborah Chuma (13 April 2025)
NY FM Mphamvu kwa mzika