“Poyamba ndisanayambe zonse ndikufuna ndipepese m’modzi mwa anthu omwe akufuna kupikisana nawo kuno a Peter Gamula kamba kotaya agogo awo dzulo omwe alowa m’manda posachedwapa”,anatero a Chilapondwa.
A Peter Gamula ndi m’modzi mwa anthu omwe akuyembekezeka kupikisana ndi a Ulemu Chilapondwa kudera la Ntchisi South Constituency.
Popitilira a Chilapondwa anati iwo ndi okondwa tsopano kuti ntchito yomanga msewu wa Malomo -Ntchisi -Dzaleka road ulimakati,komanso anati iye nthawi yomwe ali phungu wa Congress wapanga zitukuko zambili mwazina ndi ma ularo odutsa 30.
Olemba: Chifuniro Chikaphonya
spɐ puɐ sʇɥƃısuı əəS
:suoıʇɔɐəɹ llɐ
22